Doloto wachinyengo Clifford Chimtengo anapeleka mankhwala osakhalabwino kwa anthu anayi m’mudzi wa Joshua m’boma la Ntchisi. Elise Kapolo (kumam’zere) ndi amuna awo bambo Bizaliele. Dotoloyo anawanamiza anthu am’mudziwo kuti iye ndi dotolo ndipo amagwira ntchito ku chipata cha Queens mum’zinda wa Blantyre. kenako dotoloyu anapereka mankhwala kwa anthu anayi ndipo patapita ma ola angapo anthu anayiwa […]
↧