Mzika yaku Ameriaka Ya zaka 47 yomwe imapanga bisinesi ya phedwa ku nyumba yake m’bola ala Nkahatabay lachisanu sabala latha pa 20 july, 2018. Omwalirayu amatchedwa Michael James Maglioli ndipo kwawo ndiku Massachusetts ndipo adaphedwa ku nyumba yake yomwe ili m’mbali mwa nyanja ya Malawi. M’neneri wa polisi Cecilia Mfune wanena kuti Michael amagulitsa mowa […]
↧