Apolisi m’boma la Dowa akusaka zimbalangondo zosadziwika zomwe zapha gogo wachizimayi wa zaka 94 zakubadwa m’mudzi mwa Chilomba, mfumu yaikulu Msakambewa. Malingana ndi M’neneri wa polisi Sergeant Richard Mwakayoka Kaponda, adanena kuti malemuwa dzinalawo ndi Mai Talius Kwenda omwe adawapeza ataphedwa mudimba pa malo wena m’mudzi mwa Chilomba. Powonjezera Akaponda adauza mtolankhani wathu kuti Mayi […]
↧