Anyamata akabaza omwe amachita ziwonesero kamba kosakondwa ndi zoti azilipila sonkho pamwezi awanjata m’boma la Salima. Anyamata okwana 5 awamanga Ku Salima kamba kosalipila ndalama ya sonkho womwe amadula pamwezi kamba kopanga bisinesi ya kabaza Anyamata anjinga zakabazawa mwezi uliwose amapeleka K3500 Ku Boma ndicholinga Boma lizigwirisa ndalamayi pa nkhani zachitukuko. Akabaza anadandaula kuti ndikovuta […]
↧