Apolisi mu m’zinda wa Blantyre amanga nyamata wa zaka 22 kamba adamenya bambo ake mpaka kuwapha pa nkhani ya Mango. Potsimikizira nkhaniyi, M’neneri wa Polisi Sub Inspector Augustus Nkhwazi yemwe wanena kuti nyamatayi dzina lake ndi Arthur Maliro ndipo wapha bambo ake odziwika ndi dzina loti George Maliro ndipo adali ndi zaka 58. Malingana ndi […]
↧