A police ku Mzuzu akusungira m`chitokosi msing`anga wa zaka makumi awiri ndi zisanu pa mulandu ogona ndi msungwana wa zaka khumi ndi zitatu. Msing`angayi ndi Charles Muwa yemwe amachokera m`mudzi mwa Kulola mfumu yaikulu Mkanda M`boma la Mulanje. Wachiwiri kwa M`neneri wa apolisi ku Mzuzu, Cecilia Mfune wati msungwanayi anachoka ku Ekwendeni loweruka komwe amakhala […]
↧