Polisi ya kanengo ku Lilongwe ikusungira mchitokosi mzim`bambo wa zaka makumi awiri ndi zitatu (23) pa mlandu wokupha mzim`bambo nzake wa zaka makumi atatu ndi zisanu (35) kamba ka mkazi. Wachiwiri kwa ofalitsa nkhani pa polisi ya kanengo, Esther Mkwanda wati mzim`bamboyu yemwe dzina lake ndi Gift Sitina anabaya a Austin Chirombo lachinayi lapitali m`mudzi […]
↧