Apolisi ku Blantyre akusungira mchitokosi m`zibambo wa zaka makumi atatu ndi chimodzi (31) yemwe amagulitsa kanyenya wa nyama pa msika wa zingwangwa chifukwa chobaya wa bizinesi mzake. Mzibamboyu yemwe amatchedwa Mabvuto Kamkwecha Mwale anapalamula mulanduwu pa 23 Disembala chaka chomwechino. Malinga ndi ofalitsa nkhani wa polisi ku Blanytre a Augustus Nkhwazi, pa tsikuli a Mwale […]
↧